...Boma la Mozambique Lapempha Mzika Zake Kuti Zibwelere Kwawo. Boma la Mozambique lapempha mzika zake zomwe zidathawa zipolowe zokhudza chisankho ndipo zikukhala m'dziko muno kuti zibwelere kwawo. Mtsogoleri wa Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi…