Top Latest News & Reports

Akuluakuluwa saadalekere pompo koma kukhotanso ku Kampu ya Nyamithuthu, yomwe ikusunga maanja pafupifupi 2,000 omwe adathawa zipolowe m’dziko la Mozambique. Uku anacheza ndi anthu akuluakulu komanso ana (omwe anawapeza akusewera mpira ndi masewero osiyanasiyana), kumva…
Motsogozedwa ndi Mkulu wa Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi M’busa Charles Kalemba, akuluakulu ochokera ku ofesi za a Kazembe a maiko a Britain komanso United States kuno ku Malawi Lachinayi (pa 9 January, 2025)…
Wachiwiri kwa Kazembe wa Dziko la Britain kuno ku Malawi a Olympia Wereko-Brobby wati ndi wokhutira ndi mmene Boma la Malawi kudzera ku Nthambi Yoona za Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi (DoDMA) ndi abwenzi ake akulimbikitsira ntchito…

Visitors Counter

1040306
Today
Yesterday
This Week
Last Week
This Month
Last Month
All days
243
1672
3650
1027374
24263
22737
1040306

Your IP: 18.97.14.88
2025-01-22 05:22